Genesis 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu atatero, anazidalitsa kuti: “Muswane, muchuluke, mudzaze nyanja zonse.+ Ndipo zolengedwa zouluka zichuluke padziko lapansi.” Salimo 144:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nkhokwe zathu ndi zodzaza ndi zakudya zosiyanasiyana.+Nkhosa zathu zikuswana kukhala masauzandemasauzande. Nkhosa imodzi ikukhala masauzande 10 m’misewu.
22 Mulungu atatero, anazidalitsa kuti: “Muswane, muchuluke, mudzaze nyanja zonse.+ Ndipo zolengedwa zouluka zichuluke padziko lapansi.”
13 Nkhokwe zathu ndi zodzaza ndi zakudya zosiyanasiyana.+Nkhosa zathu zikuswana kukhala masauzandemasauzande. Nkhosa imodzi ikukhala masauzande 10 m’misewu.