Genesis 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero, Yehova anamva chisoni+ kuti anapanga anthu padziko lapansi, ndipo zinam’pweteka kwambiri mumtima.+
6 Chotero, Yehova anamva chisoni+ kuti anapanga anthu padziko lapansi, ndipo zinam’pweteka kwambiri mumtima.+