Genesis 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Mulungu anati: “Kukhale zounikira kuthambo kuti zilekanitse usana ndi usiku+ ndipo zikhale zizindikiro, komanso kuti zisonyeze nyengo ndi masiku ndi zaka.+ Mlaliki 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’badwo umapita+ ndipo m’badwo wina umabwera,+ koma dziko lapansi lidzakhalapobe mpaka kalekale.*+ Yeremiya 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Yehova wanena kuti, ‘Ngati anthu inu mungathe kuphwanya pangano langa loti kukhale usana ndi pangano langa loti kukhale usiku, kuti usana ndi usiku zisafike pa nthawi yake,+
14 Kenako Mulungu anati: “Kukhale zounikira kuthambo kuti zilekanitse usana ndi usiku+ ndipo zikhale zizindikiro, komanso kuti zisonyeze nyengo ndi masiku ndi zaka.+
20 “Yehova wanena kuti, ‘Ngati anthu inu mungathe kuphwanya pangano langa loti kukhale usana ndi pangano langa loti kukhale usiku, kuti usana ndi usiku zisafike pa nthawi yake,+