Genesis 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo ndikupanga pangano ndi iwe. Iweyo udzalowe m’chingalawacho limodzi ndi ana ako, mkazi wako, ndi akazi a ana ako.+ Genesis 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana a Nowa+ amene anatuluka m’chingalawa anali Semu, Hamu ndi Yafeti. Pambuyo pake, Hamu anakhala tate wake wa Kanani.+
18 Ndipo ndikupanga pangano ndi iwe. Iweyo udzalowe m’chingalawacho limodzi ndi ana ako, mkazi wako, ndi akazi a ana ako.+
18 Ana a Nowa+ amene anatuluka m’chingalawa anali Semu, Hamu ndi Yafeti. Pambuyo pake, Hamu anakhala tate wake wa Kanani.+