Genesis 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nowa anakwanitsa zaka 500. Pambuyo pake iye anabereka Semu,+ Hamu+ ndi Yafeti.+ Genesis 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Nowa analowa m’chingalawacho, limodzi ndi ana ake aamuna, mkazi wake, ndi akazi a ana ake. Iwo analowamo madzi achigumula asanayambe.+ Genesis 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano nayi mbiri ya ana a Nowa,+ omwe ndi Semu, Hamu ndi Yafeti. Pambuyo pa chigumula, iwowa anayamba kubereka ana.+
7 Pamenepo Nowa analowa m’chingalawacho, limodzi ndi ana ake aamuna, mkazi wake, ndi akazi a ana ake. Iwo analowamo madzi achigumula asanayambe.+
10 Tsopano nayi mbiri ya ana a Nowa,+ omwe ndi Semu, Hamu ndi Yafeti. Pambuyo pa chigumula, iwowa anayamba kubereka ana.+