Genesis 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pambuyo pake, Abulamu anasamutsa hema wake kumeneko. Kuyambira pa nthawi imeneyi, iye ankangokhalira kumanga ndi kusamutsa msasa, kulowera ku Negebu.+ Genesis 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Abulahamu anasamutsa msasa wake+ n’kupita kudziko la Negebu. Kenako anakakhala monga mlendo ku Gerari+ pakati pa Kadesi+ ndi Shura.+
9 Pambuyo pake, Abulamu anasamutsa hema wake kumeneko. Kuyambira pa nthawi imeneyi, iye ankangokhalira kumanga ndi kusamutsa msasa, kulowera ku Negebu.+
20 Tsopano Abulahamu anasamutsa msasa wake+ n’kupita kudziko la Negebu. Kenako anakakhala monga mlendo ku Gerari+ pakati pa Kadesi+ ndi Shura.+