Salimo 115:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu ndinu amene mwadalitsidwa ndi Yehova,+Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi.+ Chivumbulutso 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye analumbira pa Iye wokhala+ ndi moyo kwamuyaya,+ amene analenga kumwamba ndi zokhala kumeneko, ndi dziko lapansi+ ndi zinthu za mmenemo,+ ndi nyanja ndi zinthu za mmenemo. Analumbira kuti: “Sipakhalanso kuchedwa ayi.+
6 Iye analumbira pa Iye wokhala+ ndi moyo kwamuyaya,+ amene analenga kumwamba ndi zokhala kumeneko, ndi dziko lapansi+ ndi zinthu za mmenemo,+ ndi nyanja ndi zinthu za mmenemo. Analumbira kuti: “Sipakhalanso kuchedwa ayi.+