Genesis 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tikulolani pokhapokha mwamuna aliyense pakati panu atadulidwa, kuti mukhale ofanana ndi ife.+ Yoswa 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawi imeneyo, Yehova anauza Yoswa kuti: “Panga timipeni tamiyala kuti udule khungu+ la ana a Isiraeli kachiwiri.” Aroma 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma Myuda ndi amene ali wotero mkati,+ ndipo mdulidwe wake ndi wa mumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo satamandidwa+ ndi anthu koma ndi Mulungu.+
2 Pa nthawi imeneyo, Yehova anauza Yoswa kuti: “Panga timipeni tamiyala kuti udule khungu+ la ana a Isiraeli kachiwiri.”
29 Koma Myuda ndi amene ali wotero mkati,+ ndipo mdulidwe wake ndi wa mumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo satamandidwa+ ndi anthu koma ndi Mulungu.+