Ekisodo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Mose anauza Yehova kuti: “Pepani Yehova, ine sinditha kulankhula, kuyambira kalekale, kapena pamene mwalankhula ndi ine mtumiki wanu. Pakuti ndimalankhula movutikira ndipo ndine wa lilime lolemera.”+ Salimo 86:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu Yehova, tcherani khutu ku pemphero langa.+Ndipo mvetserani mawu a kuchonderera kwanga.+
10 Ndiyeno Mose anauza Yehova kuti: “Pepani Yehova, ine sinditha kulankhula, kuyambira kalekale, kapena pamene mwalankhula ndi ine mtumiki wanu. Pakuti ndimalankhula movutikira ndipo ndine wa lilime lolemera.”+