Genesis 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Munthu ameneyu sadzakhala wolowa nyumba yako ayi, koma munthu amene adzatuluke mwa iwe ndi amene adzakhale wolowa nyumba yako.”+ Yohane 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Komanso, kapolo sakhala m’banjamo kwamuyaya, mwana ndiye amakhalamo kwamuyaya.+ Agalatiya 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ngakhale zili choncho, kodi Malemba amati chiyani? “Thamangitsani mdzakaziyu pamodzi ndi mwana wakeyu pano, pakuti sizingatheke mwana wa mdzakazi kudzakhala wolandira cholowa pamodzi ndi mwana wa mkazi waufulu.”+
4 Pamenepo Yehova anamuuza kuti: “Munthu ameneyu sadzakhala wolowa nyumba yako ayi, koma munthu amene adzatuluke mwa iwe ndi amene adzakhale wolowa nyumba yako.”+
30 Ngakhale zili choncho, kodi Malemba amati chiyani? “Thamangitsani mdzakaziyu pamodzi ndi mwana wakeyu pano, pakuti sizingatheke mwana wa mdzakazi kudzakhala wolandira cholowa pamodzi ndi mwana wa mkazi waufulu.”+