Genesis 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zidzatero chifukwa Abulahamu anamvera mawu anga, ndipo anachita zofuna zanga ndi kusunga malamulo anga onse.”+ Salimo 119:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Ndinafulumira ndipo sindinazengereze+Kusunga malamulo anu.+
5 Zidzatero chifukwa Abulahamu anamvera mawu anga, ndipo anachita zofuna zanga ndi kusunga malamulo anga onse.”+