Genesis 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Farao anamusamalira bwino Abulamu chifukwa cha mkazi wake, moti anamupatsa nkhosa, ng’ombe ndi abulu. Anamupatsanso antchito aamuna ndi aakazi, komanso abulu aakazi ndi ngamila.+
16 Farao anamusamalira bwino Abulamu chifukwa cha mkazi wake, moti anamupatsa nkhosa, ng’ombe ndi abulu. Anamupatsanso antchito aamuna ndi aakazi, komanso abulu aakazi ndi ngamila.+