Genesis 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kanani anabereka Sidoni+ mwana wake woyamba, kenako anabereka Heti.+ Genesis 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero ana a Heti anagulitsa kwa Abulahamu malowo ndi phanga limene linali pamenepo, ndipo mkazi wake anamuika m’manda kumeneko.+
20 Chotero ana a Heti anagulitsa kwa Abulahamu malowo ndi phanga limene linali pamenepo, ndipo mkazi wake anamuika m’manda kumeneko.+