Genesis 49:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kumeneko n’kumene anaika Abulahamu ndi mkazi wake Sara.+ N’kumene anaika Isaki ndi Rabeka mkazi wake,+ ndipo n’kumene ndinaika Leya. Machitidwe 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komatu sanam’patse cholowa chilichonse mmenemu ayi, ngakhale kadera kochepetsetsa.+ Koma anamulonjeza kuti adzamupatsa dzikoli monga cholowa chake,+ ndi cha mbewu yake,+ ngakhale kuti pa nthawiyo n’kuti alibe mwana.+
31 Kumeneko n’kumene anaika Abulahamu ndi mkazi wake Sara.+ N’kumene anaika Isaki ndi Rabeka mkazi wake,+ ndipo n’kumene ndinaika Leya.
5 Komatu sanam’patse cholowa chilichonse mmenemu ayi, ngakhale kadera kochepetsetsa.+ Koma anamulonjeza kuti adzamupatsa dzikoli monga cholowa chake,+ ndi cha mbewu yake,+ ngakhale kuti pa nthawiyo n’kuti alibe mwana.+