Ezekieli 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndinakuveka ndolo ya pamphuno+ ndi ndolo za m’makutu*+ ndiponso chisoti chokongola pamutu pako.+