Genesis 24:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Atatero ndinamufunsa kuti, ‘Kodi ndiwe mwana wa ndani?’+ Iye anandiyankha kuti, ‘Ine bambo anga ndi a Betuele. Bambo awo ndi a Nahori, ndipo mayi awo ndi a Milika.’ Ndiyeno ndinamuveka ndolo ya pamphuno ndi zibangili m’mikono yake.+ Yesaya 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 mphete zovala m’zala, mphete zovala pamphuno,+
47 Atatero ndinamufunsa kuti, ‘Kodi ndiwe mwana wa ndani?’+ Iye anandiyankha kuti, ‘Ine bambo anga ndi a Betuele. Bambo awo ndi a Nahori, ndipo mayi awo ndi a Milika.’ Ndiyeno ndinamuveka ndolo ya pamphuno ndi zibangili m’mikono yake.+