Genesis 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako, ngamila zija zitatha kumwa, mlendoyo anatenga ndolo yagolide yovala pamphuno+ yolemera hafu ya sekeli, ndi zibangili ziwiri+ zagolide zoti Rabeka azivala m’mikono, zolemera masekeli 10, Ezekieli 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndinakuvekanso zokongoletsera ndi zibangili+ m’manja mwako ndipo ndinakuveka mkanda+ m’khosi mwako.
22 Kenako, ngamila zija zitatha kumwa, mlendoyo anatenga ndolo yagolide yovala pamphuno+ yolemera hafu ya sekeli, ndi zibangili ziwiri+ zagolide zoti Rabeka azivala m’mikono, zolemera masekeli 10,
11 Ndinakuvekanso zokongoletsera ndi zibangili+ m’manja mwako ndipo ndinakuveka mkanda+ m’khosi mwako.