Yeremiya 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kodi namwali angaiwale zodzikongoletsera? Kodi mkwatibwi angaiwale lamba wake wa pachifuwa? Koma anthu anga andiiwala kwa masiku osawerengeka.+ Ezekieli 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndinakuvekanso zokongoletsera ndi zibangili+ m’manja mwako ndipo ndinakuveka mkanda+ m’khosi mwako.
32 Kodi namwali angaiwale zodzikongoletsera? Kodi mkwatibwi angaiwale lamba wake wa pachifuwa? Koma anthu anga andiiwala kwa masiku osawerengeka.+
11 Ndinakuvekanso zokongoletsera ndi zibangili+ m’manja mwako ndipo ndinakuveka mkanda+ m’khosi mwako.