Genesis 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako, ngamila zija zitatha kumwa, mlendoyo anatenga ndolo yagolide yovala pamphuno+ yolemera hafu ya sekeli, ndi zibangili ziwiri+ zagolide zoti Rabeka azivala m’mikono, zolemera masekeli 10, Yesaya 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndolo,* zibangili za m’manja, nsalu zofunda,+
22 Kenako, ngamila zija zitatha kumwa, mlendoyo anatenga ndolo yagolide yovala pamphuno+ yolemera hafu ya sekeli, ndi zibangili ziwiri+ zagolide zoti Rabeka azivala m’mikono, zolemera masekeli 10,