Genesis 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma asanamalize kulankhula,+ anangoona Rabeka mwana wa Betuele+ akutuluka mumzindawo. Betuele anali mwana wa Milika,+ ndipo Milika anali mkazi wa Nahori,+ m’bale wake wa Abulahamu. Rabekayo anali atasenza mtsuko paphewa pake.+
15 Koma asanamalize kulankhula,+ anangoona Rabeka mwana wa Betuele+ akutuluka mumzindawo. Betuele anali mwana wa Milika,+ ndipo Milika anali mkazi wa Nahori,+ m’bale wake wa Abulahamu. Rabekayo anali atasenza mtsuko paphewa pake.+