1 Mafumu 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma mitengo yonyamulirayo+ inali yaitali, moti nsonga zake zinkaoneka kuchokera ku Malo Oyera kutsogolo kwa chipinda chamkati, koma sizinali kuoneka kunja. Mitengo yonyamulirayo ikadali pomwepo mpaka lero.+
8 Koma mitengo yonyamulirayo+ inali yaitali, moti nsonga zake zinkaoneka kuchokera ku Malo Oyera kutsogolo kwa chipinda chamkati, koma sizinali kuoneka kunja. Mitengo yonyamulirayo ikadali pomwepo mpaka lero.+