Ekisodo 37:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Analikuta ndi golide woyenga bwino, ndipo anapanga mkombero wagolide kuzungulira tebulo lonselo.+