Ekisodo 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ulikute ndi golide woyenga bwino, ndipo upange mkombero wagolide kuzungulira tebulo lonselo.+