Ekisodo 37:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choikapo nyalechi chinali ndi nthambi 6. Kumbali ina kunatuluka nthambi zitatu, ndipo kumbali inayo kunatulukanso nthambi zitatu.+
18 Choikapo nyalechi chinali ndi nthambi 6. Kumbali ina kunatuluka nthambi zitatu, ndipo kumbali inayo kunatulukanso nthambi zitatu.+