Ekisodo 25:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choikapo nyalecho chikhale ndi nthambi 6, kumbali ina kutuluke nthambi zitatu, ndipo kumbali inayo kutulukenso nthambi zitatu.+
32 Choikapo nyalecho chikhale ndi nthambi 6, kumbali ina kutuluke nthambi zitatu, ndipo kumbali inayo kutulukenso nthambi zitatu.+