Numeri 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choikapo nyalecho chinali chooneka motere kapangidwe kake: Chinali chosula, chagolide. Chinasulidwa kuchokera kutsinde lake mpaka kumaluwa ake.+ Anachisula malinga ndi chitsanzo chimene Yehova anaonetsa+ Mose m’masomphenya.
4 Choikapo nyalecho chinali chooneka motere kapangidwe kake: Chinali chosula, chagolide. Chinasulidwa kuchokera kutsinde lake mpaka kumaluwa ake.+ Anachisula malinga ndi chitsanzo chimene Yehova anaonetsa+ Mose m’masomphenya.