Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mukapange chihema chopatulika ndi ziwiya zake mogwirizana ndendende ndi zonse zimene ndikukusonyeza.+

  • Ekisodo 25:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Uonetsetse kuti wazipanga motsatira chitsanzo chimene wasonyezedwa m’phiri.+

  • 1 Mbiri 28:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Panalinso mapulani a kamangidwe ka zonse zimene anauzidwa kudzera mwa mzimu+ zokhudza mabwalo+ a nyumba ya Yehova, zipinda zonse zodyeramo+ kuzungulira kachisi, chuma cha nyumba ya Mulungu woona, ndi chuma cha zinthu zimene anaziyeretsa kukhala zopatulika.+

  • 1 Mbiri 28:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Zonsezi zalembedwa+ chifukwa chakuti dzanja la Yehova linali pa ine, ndipo anandithandiza kumvetsa mbali zake zonse za mapulani a kamangidwe kake.”+

  • Aheberi 8:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma amuna amenewo akuchita utumiki wopatulikawo m’chifaniziro+ ndi mu mthunzi+ wa zinthu zakumwamba. Izi zinaonekera mu lamulo limene Mulungu anapatsa Mose, atatsala pang’ono kumanga chihema.+ Lamulo lake linali lakuti:+ “Uonetsetse kuti wapanga zinthu zonse motsatira chitsanzo chimene wasonyezedwa m’phiri.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena