Ekisodo 25:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Uonetsetse kuti wazipanga motsatira chitsanzo chimene wasonyezedwa m’phiri.+ Ekisodo 26:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Umange chihema chopatulikacho motsatira pulani imene ndakuonetsa m’phiri.+ Numeri 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choikapo nyalecho chinali chooneka motere kapangidwe kake: Chinali chosula, chagolide. Chinasulidwa kuchokera kutsinde lake mpaka kumaluwa ake.+ Anachisula malinga ndi chitsanzo chimene Yehova anaonetsa+ Mose m’masomphenya. Machitidwe 7:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 “Makolo athuwo anali ndi chihema cha umboni m’chipululu. Anachipanga potsatira malangizo amene Mulungu anapereka pamene anali kulankhula ndi Mose. Mulungu anauza Mose kuti apange chihemacho molingana ndi chithunzi chimene anachiona.+
4 Choikapo nyalecho chinali chooneka motere kapangidwe kake: Chinali chosula, chagolide. Chinasulidwa kuchokera kutsinde lake mpaka kumaluwa ake.+ Anachisula malinga ndi chitsanzo chimene Yehova anaonetsa+ Mose m’masomphenya.
44 “Makolo athuwo anali ndi chihema cha umboni m’chipululu. Anachipanga potsatira malangizo amene Mulungu anapereka pamene anali kulankhula ndi Mose. Mulungu anauza Mose kuti apange chihemacho molingana ndi chithunzi chimene anachiona.+