Ekisodo 36:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anaika zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe pansalu imodzi, ndipo anaikanso zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe m’mphepete mwa nsalu ina imene inali polumikizirana nsalu ziwirizo. Zingwezo zinakhala moyang’anizana.+
12 Anaika zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe pansalu imodzi, ndipo anaikanso zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe m’mphepete mwa nsalu ina imene inali polumikizirana nsalu ziwirizo. Zingwezo zinakhala moyang’anizana.+