Ekisodo 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndipo ana a Isiraeli anachita mogwirizana ndi mawu onse amene Mose anawauza, motero anapempha Aiguputo zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala.+ Ekisodo 36:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndiyeno anakuta mafelemuwo ndi golide, ndipo anapanga mphete zake zagolide zolowetsamo mipiringidzo. Mipiringidzoyo anaikuta ndi golide.+
35 Ndipo ana a Isiraeli anachita mogwirizana ndi mawu onse amene Mose anawauza, motero anapempha Aiguputo zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala.+
34 Ndiyeno anakuta mafelemuwo ndi golide, ndipo anapanga mphete zake zagolide zolowetsamo mipiringidzo. Mipiringidzoyo anaikuta ndi golide.+