Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 38:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako anapanga ziwiya zonse zogwiritsa ntchito paguwalo. Anapanga ndowa, mafosholo, mbale zolowa, mafoloko aakulu, ndi zopalira moto. Ziwiya zake zonse anazipanga ndi mkuwa.+

  • Levitiko 16:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Kenako iye azitenga chofukizira+ chodzaza ndi makala amoto ochokera paguwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova. Azitenganso zofukiza zonunkhira zabwino kwambiri+ zokwana manja awiri+ odzaza, ndi kulowa nazo kuchipinda, kuseri kwa nsalu yotchinga.*+

  • 1 Mafumu 7:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 ndowa, mafosholo, mbale zolowa, ndi ziwiya zina zonse.+ Hiramu anapanga zinthu zimenezi ndi mkuwa wonyezimira. Anapangira Mfumu Solomo kuti aziike m’nyumba ya Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena