Ekisodo 39:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno anasula golide kukhala wopyapyala kwambiri, ndipo anam’lenzalenza kukhala ngati tizingwe kuti apetere limodzi ndi ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wabwino kwambiri.+
3 Ndiyeno anasula golide kukhala wopyapyala kwambiri, ndipo anam’lenzalenza kukhala ngati tizingwe kuti apetere limodzi ndi ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wabwino kwambiri.+