Ekisodo 39:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo miyalayo anailowetsa pansalu za m’mapewa za efodi kuti ikhale chikumbutso+ kwa ana a Isiraeli, monga mmene Yehova analamulira Mose.
7 Ndipo miyalayo anailowetsa pansalu za m’mapewa za efodi kuti ikhale chikumbutso+ kwa ana a Isiraeli, monga mmene Yehova analamulira Mose.