Ekisodo 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo ulowetse miyala iwiriyo pansalu za m’mapewa za efodi kuti ikhale miyala ya chikumbutso cha ana a Isiraeli.+ Poonekera kwa Yehova, Aroni azidzanyamula mayina awo pansalu ziwiri za m’mapewa ake kuti chikhale chikumbutso.
12 Ndipo ulowetse miyala iwiriyo pansalu za m’mapewa za efodi kuti ikhale miyala ya chikumbutso cha ana a Isiraeli.+ Poonekera kwa Yehova, Aroni azidzanyamula mayina awo pansalu ziwiri za m’mapewa ake kuti chikhale chikumbutso.