Ekisodo 39:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akachipinda pakati chinali chofanana mbali zonse zinayi. Chovala pachifuwacho anachipanga kuti akachipinda pakati, m’litali mwake chizikhala chikhatho* chimodzi ndipo m’lifupi mwake chikhatho chimodzi.+
9 Akachipinda pakati chinali chofanana mbali zonse zinayi. Chovala pachifuwacho anachipanga kuti akachipinda pakati, m’litali mwake chizikhala chikhatho* chimodzi ndipo m’lifupi mwake chikhatho chimodzi.+