Ekisodo 39:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anapanganso zoikamo miyala ziwiri zagolide ndi mphete ziwiri zagolide, ndipo anaika mphete ziwirizo m’makona awiri a chovala pachifuwacho.+
16 Anapanganso zoikamo miyala ziwiri zagolide ndi mphete ziwiri zagolide, ndipo anaika mphete ziwirizo m’makona awiri a chovala pachifuwacho.+