Ekisodo 39:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atatero anapanga mphete ziwiri zagolide ndi kuziika m’makona awiri a chovala pachifuwa, kumbali yopindira mkati yokhudzana ndi efodi.+
19 Atatero anapanga mphete ziwiri zagolide ndi kuziika m’makona awiri a chovala pachifuwa, kumbali yopindira mkati yokhudzana ndi efodi.+