Ekisodo 39:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kenako anapanganso mabelu agolide woyenga bwino ndi kuwaika pakati pa makangaza,+ kuzungulira mpendero wa m’munsi wa malaya odula manjawo, pakati pa makangaza.
25 Kenako anapanganso mabelu agolide woyenga bwino ndi kuwaika pakati pa makangaza,+ kuzungulira mpendero wa m’munsi wa malaya odula manjawo, pakati pa makangaza.