Ekisodo 39:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anaika belu ndi khangaza,* belu ndi khangaza, kuzungulira mpendero wa m’munsi mwa malaya odula manja.+ Malayawo ndi oti azivala potumikira, monga mmene Yehova analamulira Mose.
26 Anaika belu ndi khangaza,* belu ndi khangaza, kuzungulira mpendero wa m’munsi mwa malaya odula manja.+ Malayawo ndi oti azivala potumikira, monga mmene Yehova analamulira Mose.