Ekisodo 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo Aroni anawauza mawu onse amene Yehova anauza Mose,+ ndipo iye anachita zizindikiro+ pamaso pa anthuwo.
30 Pamenepo Aroni anawauza mawu onse amene Yehova anauza Mose,+ ndipo iye anachita zizindikiro+ pamaso pa anthuwo.