Ekisodo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako iye anati: “Iponye pansi.” Anaiponya pansi ndipo inasanduka njoka.+ Pamenepo Mose anayamba kuthawa. Ekisodo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Yehova anamuuzanso kuti: “Lowetsa dzanja lako m’malaya pachifuwa.” Choncho Mose analowetsa dzanja lake m’malaya. Koma politulutsa, dzanja lakelo linali litachita khate, ndipo linaoneka loyera kwambiri ngati chipale chofewa.+ Ekisodo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komabe ngati sakakhulupirira zizindikiro ziwirizi ndi kumvera mawu ako,+ ukatenge madzi a mumtsinje wa Nailo n’kuwathira panthaka youma. Ndipo madziwo, amene ukatenge mumtsinje wa Nailo, adzasanduka magazi panthakapo. Ndithu adzasanduka magazi.”+
3 Kenako iye anati: “Iponye pansi.” Anaiponya pansi ndipo inasanduka njoka.+ Pamenepo Mose anayamba kuthawa.
6 Kenako Yehova anamuuzanso kuti: “Lowetsa dzanja lako m’malaya pachifuwa.” Choncho Mose analowetsa dzanja lake m’malaya. Koma politulutsa, dzanja lakelo linali litachita khate, ndipo linaoneka loyera kwambiri ngati chipale chofewa.+
9 Komabe ngati sakakhulupirira zizindikiro ziwirizi ndi kumvera mawu ako,+ ukatenge madzi a mumtsinje wa Nailo n’kuwathira panthaka youma. Ndipo madziwo, amene ukatenge mumtsinje wa Nailo, adzasanduka magazi panthakapo. Ndithu adzasanduka magazi.”+