Levitiko 7:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “‘Mwendo wakumbuyo wa kudzanja lamanja muziupereka kwa wansembe monga gawo lopatulika+ lochokera pansembe zanu zachiyanjano. Levitiko 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma Aroni anaweyula*+ cha uku ndi uku ngangazo ndi mwendo wakumbuyo wa kudzanja lamanja pamaso pa Yehova, monga mmene Mose analamulira. Numeri 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Uzitenga nyama yake kuti ikhale yako, mofanana ndi nganga ya nsembe yoweyula, komanso mwendo wam’mbuyo wakumanja.+
32 “‘Mwendo wakumbuyo wa kudzanja lamanja muziupereka kwa wansembe monga gawo lopatulika+ lochokera pansembe zanu zachiyanjano.
21 Koma Aroni anaweyula*+ cha uku ndi uku ngangazo ndi mwendo wakumbuyo wa kudzanja lamanja pamaso pa Yehova, monga mmene Mose analamulira.
18 Uzitenga nyama yake kuti ikhale yako, mofanana ndi nganga ya nsembe yoweyula, komanso mwendo wam’mbuyo wakumanja.+