Ekisodo 29:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pa nkhosa yolongera Aroni ndi ana ake unsembe,+ upatule nganga+ ya nsembe yoweyula imene anaweyula, ndi mwendo wa gawo lopatulika umene anapereka. Levitiko 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atatero anaika zonsezi m’manja mwa Aroni ndi m’manja mwa ana ake n’kuyamba kuziweyula* uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+
27 Pa nkhosa yolongera Aroni ndi ana ake unsembe,+ upatule nganga+ ya nsembe yoweyula imene anaweyula, ndi mwendo wa gawo lopatulika umene anapereka.
27 Atatero anaika zonsezi m’manja mwa Aroni ndi m’manja mwa ana ake n’kuyamba kuziweyula* uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+