Levitiko 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno Mose anazitenga m’manja mwawo n’kuzitentha paguwa lansembe pamwamba pa nsembe yopsereza.+ Zimenezi zinali nsembe yowalongera unsembe,+ yafungo lokhazika mtima pansi.+ Inali nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.+ Aefeso 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo yendanibe m’chikondi,+ monganso Khristu anakukondani+ n’kudzipereka yekha chifukwa cha inu. Iye anadzipereka yekha monga chopereka+ ndiponso monga nsembe yafungo lokoma kwa Mulungu.+
28 Ndiyeno Mose anazitenga m’manja mwawo n’kuzitentha paguwa lansembe pamwamba pa nsembe yopsereza.+ Zimenezi zinali nsembe yowalongera unsembe,+ yafungo lokhazika mtima pansi.+ Inali nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.+
2 ndipo yendanibe m’chikondi,+ monganso Khristu anakukondani+ n’kudzipereka yekha chifukwa cha inu. Iye anadzipereka yekha monga chopereka+ ndiponso monga nsembe yafungo lokoma kwa Mulungu.+