Levitiko 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Chotero mukhale pakhomo la chihema chokumanako usana ndi usiku kwa masiku 7.+ Ndipo muyenera kuchita ulonda umene Yehova walamula,+ kuti musafe. Chifukwa n’zimene ndalamulidwa.” Levitiko 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano pa tsiku la 8,+ Mose anaitana Aroni, ana ake ndi akulu a Isiraeli.
35 Chotero mukhale pakhomo la chihema chokumanako usana ndi usiku kwa masiku 7.+ Ndipo muyenera kuchita ulonda umene Yehova walamula,+ kuti musafe. Chifukwa n’zimene ndalamulidwa.”