Ekisodo 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma musadzasiye nyama iliyonse kuti ifike m’mawa. Iliyonse yotsala kufika m’mawa mudzaipsereze pamoto.+ Levitiko 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo nyama ndi mkate zotsala muzitenthe ndi moto.+
10 Koma musadzasiye nyama iliyonse kuti ifike m’mawa. Iliyonse yotsala kufika m’mawa mudzaipsereze pamoto.+