Levitiko 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nyama ya nsembe zachiyanjano zoperekedwa monga nsembe yoyamikira aziidya pa tsiku limene waipereka. Asasunge iliyonse ya nyamayo kufika m’mawa.+ Levitiko 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Muziidya pa tsiku lomwelo.+ Musasiyeko iliyonse kufikira m’mawa.+ Ine ndine Yehova. Deuteronomo 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Usapezeke ndi mtanda wa ufa wokanda wokhala ndi chofufumitsa m’dziko lako lonse masiku 7.+ Nyama iliyonse imene wapereka nsembe madzulo, pa tsiku loyamba, isagone mpaka m’mawa.+
15 Nyama ya nsembe zachiyanjano zoperekedwa monga nsembe yoyamikira aziidya pa tsiku limene waipereka. Asasunge iliyonse ya nyamayo kufika m’mawa.+
4 Usapezeke ndi mtanda wa ufa wokanda wokhala ndi chofufumitsa m’dziko lako lonse masiku 7.+ Nyama iliyonse imene wapereka nsembe madzulo, pa tsiku loyamba, isagone mpaka m’mawa.+