Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 35:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Zitatero, Yakobo anaimika mwala wachikumbutso pamalo pamene anali kulankhula nayepo,+ kenako pamwalawo anathirapo nsembe yachakumwa ndi mafuta.+

  • Levitiko 23:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Popereka nsembe imeneyi muziperekanso nsembe yambewu. Nsembeyo izikhala ufa wosalala wothira mafuta, muyezo wake magawo awiri mwa magawo 10 a muyezo wa efa, kuti ikhale nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova, yafungo lokhazika mtima pansi. Muziperekanso vinyo wa nsembe yachakumwa, muyezo wake gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini.*

  • Afilipi 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ngakhale kuti ndikudzipereka ngati nsembe yachakumwa imene ikuthiridwa+ pansembe+ ndi pa ntchito yotumikira anthu imene chikhulupiriro chakupatsani,+ ndine wokondwa ndipo ndikukondwera+ ndi inu nonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena