Numeri 3:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 utenge masekeli* asanu pa munthu aliyense.+ Utenge muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Sekeli limodzi likukwana magera 20.+
47 utenge masekeli* asanu pa munthu aliyense.+ Utenge muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Sekeli limodzi likukwana magera 20.+