Ekisodo 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwe uzimuuza zonse zimene ndizikulamula,+ koma Aroni m’bale wako azikulankhulira kwa Farao,+ ndipo adzaloladi ana a Isiraeli kuchoka m’dziko lake.+
2 Iwe uzimuuza zonse zimene ndizikulamula,+ koma Aroni m’bale wako azikulankhulira kwa Farao,+ ndipo adzaloladi ana a Isiraeli kuchoka m’dziko lake.+